Smallholder tea poster -12Sep11.cdr - Sustainable Agriculture Training

Kasamalidwe ka zinyalala Zomwe zinatha Kawola. Kuteteza mbewu ku tizilombo (kutiana ndi matenda wotchedwa Armilaria owon
1MB Größe 3 Downloads 59 Ansichten
Ndondomeko zofunikira za ulimi oyenera - Za alimi ang'onoang'ono a tiyi Kuteteza mbewu ku tizilombo (kuthana ndi matenda wotchedwa Armilaria owononga mitengo ya tiyi)

Mtengo wa tiyi wang'aluka ndipo ukutulutsa tiufa toyera

Zulani phata lonse ndi mizu yomwe ndipo mutenthe

Kuteteza mbewu ku tizilombo (kutengulira)

Kasamalidwe ka zinyalala zomwe zimatha kuwola

Kupanga manyowa kuchokela ku zinyalala zomwe zimatha kuwola

Kuwotcha zinyalala

Kusamala madzi oyipa pakhomo

Madzi Kutengulira tiyi kuti tizilombo tisapitilire kufala. Nthambi zomwe zadulidwa zitha kugwiritsidwa ntchito pophimbira mbewu.

Tizilombo tikupitilira kuwononga tiyi

Zipangizo zozitetezela

Kupopela osaziteteza

Chovala kunkhope chotchinjiliza kuti mankhwala asakukhudzeni

Chovala choteteza ku mvula

Kupopela ndi zozitetezela

Kasungidwe ka mankhwala

Kutaya madzi mu nkhuti momwe mwabzalidwa nthochi (Dziwani izi: ngati madzi akupanga zithaphwi (sakuyenda), mukumbe dzenje ndikuikamo miyala)

Kutaya madzi oyipa kutsogolo kwa nyumba

Kutsuka zipangizo

Kutsuka zipangizo mu mtsinje kapena dziwe

Kutaya madzi ochapila mu dimba lomwe lathilidwa mankhwala

Kapena, kutaya madzi mu nkhuti yomwe muli makala

Kusamala chilengedwe

Bulugama Mtsinje ukuwuma

Kusunga mankhwala m'nyumba

Mwachitsanzo, khola lankhuku lakale mutha kulisandutsa mosungira mankhwala. Ikanimo pulasitiki mkati

M'golo wa chitsulo mutha kuusandutsa mosungira

Kasamalidwe ka zinyalala za pulasitiki ndi mabotolo Potolela a mankhwala Mabotolo opanda

Mabotolo opanda kanthu komanso zinyalala za pulasitiki zatayidwa pansi Version: June 2011

zinyalala za pulasitiki

mabotolo a mankhwala ndi zinyalala za pulasitiki, onetsetsani kuti mwazisiyanitsa (pamapeto pa zonse, otsogolera gulu watolela zonse)

Bulugama amaumitsa mitsinje ndi zitsime

Kuzula bulugama amene ali pafupi ndi mtsinje

Mtsinje wabwelera mchimake

Kuteteza nthaka kuti isakokoloke

Vuto la kukokoloka kwa nthaka

Kubzala mitengo yachilengedwe ndi nsenjere kuti muteteze nthaka komanso madzi